16 Taonani, Ine ndikutumizani inu monga nkhosa pakati pa afisi; cifukwa cace khalani ocenjera monga njoka, ndi oona mtima monga nkhunda.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:16 nkhani