Mateyu 10:17 BL92

17 Koma cenjerani ndi anthu; pakuti adzakuperekani inu kwa akuru a mlandu, nadzakukwapulani inu m'masunagoge mwao;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 10

Onani Mateyu 10:17 nkhani