25 Kumkwanira wophunzira kuti akhale monga mphunzitsi wace, ndi kapolo monga mbuye. Ngati anamucha mwini banja Beelzebule, sadzaposa kodi kuwatero apabanja ace?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:25 nkhani