26 Cifukwa cace musaopa iwo; pakuti palibe kanthu kanabvundikiridwa, kamene sikadzaululidwa; kapena kanthu kobisika, kamene sikadzadziwika.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:26 nkhani