40 8 Iye wakulandira inu, andilandira Ine, ndi wakundilandira Ine, amlandira Iye amene ananditumiza Ine.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:40 nkhani