41 9 Iye wakulandira mneneri, pa dzina la mneneri, adzalandira mphotho ya mneneri; ndipo wakulandira munthu wolungama, pa dzina la munthu wolungama, adzalandira mphotho ya munthu wolungama.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:41 nkhani