42 Ndipo 10 amenealiyense adzamwetsa mmodzi wa ang'ono awa cikho cokha ca madzi ozizira, pa dzina la wophunzira, indetu ndinena kwa inu, iye sadzataya mphotho yace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 10
Onani Mateyu 10:42 nkhani