Mateyu 11:1 BL92

1 Ndipo panali, pamene Yesu anatha kuwafotokozera ophunzira ace khumi Ndi awiri, Iye anacokera kumeneko kukaphunzitsa Ndi kulalikira m'midzi mwao.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 11

Onani Mateyu 11:1 nkhani