Mateyu 11:12 BL92

12 Ndipo kuyambira masiku a Yohane Mbatizi, kufikira tsopano lino, Ufumu wa Kumwamba uli wokangamizidwa, ndipo okangamirawo aukwatula ndi mphamvu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 11

Onani Mateyu 11:12 nkhani