Mateyu 11:7 BL92

7 Ndipo m'mene iwo analikumuka, Yesu anayambonena Ndi makamu a anthu za kwa Yohane, Munaturuka kunka kucipululu kukapenyanji? Bango logwedezeka nd: mphepo kodi?

Werengani mutu wathunthu Mateyu 11

Onani Mateyu 11:7 nkhani