22 Pomwepo anabwera naye kwa Iye munthu wogwidwa ndi ciwanda, wakhungu ndi wosalankhula; ndipo Iye anamciritsa, kotero kuti wosalankhulayo analankhula, napenya.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:22 nkhani