Mateyu 12:25 BL92

25 Ndipo Yesu anadziwa maganizo ao, nati kwa iwo, Ufumu uti wonse wogawanika pa wokha sukhalira kupasuka, ndi mudzi uti wonse kapena banja logawanika pa lokha silidzakhala;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 12

Onani Mateyu 12:25 nkhani