26 ndipo ngati Satana amaturutsa Satana, iye agawanika pa yekha; ndipo udzakhala bwanji ufumu wace?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:26 nkhani