27 Ndipo ngati Ine ndimaturutsa ziwanda ndi mphamvu yace ya Beelzebule, ana anu amaziturutsa ndi mphamvu ya yani? cifukwa cace iwo adzakhala oweruza anu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:27 nkhani