31 Cifukwa cace ndinena kwa inu, Macimo onse, ndi zonena zonse zamwano, zidzakhululukidwa kwa anthu; koma camwano ca pa Mzimu Woyera sicidzakhululukidwa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:31 nkhani