32 Ndipo amene ali yense anganenere Mwana wa munthu zoipa, adzakhululukidwa; koma amene ali yense anganenere Mzimu Woyera zoipa sadzakhululukidwa nthawi yino kapena irinkudzayo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:32 nkhani