Mateyu 12:33 BL92

33 Ukakoma mtengo, cipatso cace comwe cikoma; ukaipa mtengo, cipatso cace comwe ciipa; pakuti ndi cipatso cace mtengo udziwika.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 12

Onani Mateyu 12:33 nkhani