39 Koma Iye anayankha nati kwa iwo, Akubadwa oipa acigololo afunafuna cizindikiro; ndipo sicidzapatsidwa kwa iwo cizindikiro, komatu cizindikiro ca Yona mneneri;
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:39 nkhani