Mateyu 12:40 BL92

40 pakuti monga Yona anali m'mimba mwa cinsomba masiku atatu ndi usiku wace, comweco Mwana wa munthu adzakhala mumtima mwa dziko lapansi masiku atatu ndi usiku wace.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 12

Onani Mateyu 12:40 nkhani