49 Ndipo anatambalitsa dzanja lace pa ophunzira ace, nati, Penyani amai wanga ndi abale anga!
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:49 nkhani