50 Pakuti 6 ali yense amene adzacita cifuniro ca Atate wanga wa Kumwamba, yemweyo ndiye mbale wanga, ndi mlongo wanga, ndi amai wanga.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 12
Onani Mateyu 12:50 nkhani