Mateyu 13:12 BL92

12 Pakuti yense amene ali nazo, kudzapatsidwa kwa iye, ndimo adzakhala nazo zocuruka; koma yense amene alibe, cingakhale comwe ali naco cidzacotsedwa kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:12 nkhani