13 Cifukwa cace ndiphiphiritsira iwo m'mafanizo; cifukwa kuti akuona samaona, ndi akumva samamva, kapena samadziwitsa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:13 nkhani