14 Ndipo adzacitidwa kwa iwo mau adanenera Yesaya, amene ati.Pakumva mudzamva, ndipo simudzazindikira konse;Pakupenya mudzapenya, ndipo simudzaona konse;
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:14 nkhani