Mateyu 13:21 BL92

21 ndipo alibe mizu mwa iye, koma akhala nthawi yaing'ono; ndipo pakudza nsautso kapena zunzo cifukwa ca mau, iye akhumudwa pomwepo.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:21 nkhani