27 Ndipo anyamata ace a mwini nyumbayo anadza, nati kwa iye, Mbuye, kodi simunafesa mbeu zabwino m'munda mwanu? nanga wacokera kuti namsongoleyo?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:27 nkhani