28 Ndipo iye ananena kwa iwo, Munthu mdani wanga wacicita ici. Ndipo anyamata anati kwa iye, Kodi mufuna tsopano kuti timuke, tikamsonkhanitse uyo pamodzi?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:28 nkhani