Mateyu 13:33 BL92

33 Fanizo lina ananena kwa iwo; Ufumu wa Kumwamba uli wofanafana ndi cotupitsa mikate, cimene mkazi anacitenga, nacibisa m'miyeso itatu ya ufa, kufikira wonse unatupa.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:33 nkhani