Mateyu 13:36 BL92

36 Pomwepo Iye anasiya makamuwo, nalowa m'nyumba; ndimo ophunzira ace anadza kwa Iye, nanena, Mutitanthauzire fanizo lija la namsongole wa m'munda.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:36 nkhani