35 kuti cikacitidwe conenedwa ndi mneneri, kuti,Ndidzatsegula pakamwa panga ndi mafanizo;Ndidzaulula zinthu zobisika ciyambire kukhazikidwa kwace kwa dziko lapansi.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:35 nkhani