39 ndipo mdani amene anamfesa uwu ndiye mdierekezi: ndi kututa ndico cimariziro ca nthawi ya pansi pano; ndi otutawo ndiwo angelo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:39 nkhani