4 Ndipo m'kufesa kwace zina zinagwa m'mbali mwa njira, ndipo zinadza mbalame, nizilusira izo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:4 nkhani