Mateyu 13:5 BL92

5 Koma zina zinagwa pamiyala, pamene panalibe dothi lambiri; ndipo pomwepo zinamera, pakuti sizinakhala nalo dothi lakuya, Ndipo m'mene dzuwa linakwera zinapserera;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 13

Onani Mateyu 13:5 nkhani