43 Pomwepo olungamawo adzawalitsa monga dzuwa, mu Ufumu wa Atate wao. Amene ali ndi makutu amve.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:43 nkhani