44 Ufumu wa Kumwamba uli wofanana ndi cuma cobisika m'munda; cimene munthu anacipeza, nacibisa; ndipo m'kucikonda kwace acoka, nagulitsa zonse ali nazo, nagula munda umenewu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 13
Onani Mateyu 13:44 nkhani