13 Ndipo Yesu pakumva, anacokera kumeneko m'ngalawa, kunka ku malo acipululu pa yekha; ndipo makamu, pamene anamva, anamtsata Iye mumtunda kucokera m'midzi.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 14
Onani Mateyu 14:13 nkhani