Mateyu 14:14 BL92

14 Ndipo Iye anaturuka, naona khamu lalikuru la anthu, nacitira iwo cifundo, naciritsa akudwala ao.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 14

Onani Mateyu 14:14 nkhani