22 Ndipo onani, mkazi wa ku Kanani anaturuka m'malire, napfuula, nati, Mundicitire ine cifundo Ambuye, mwana wa Davide; mwana wanga wamkazi wagwidwa koopsa ndi ciwanda.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 15
Onani Mateyu 15:22 nkhani