23 Koma Iye sanamyankha mau amodzi. Ndipo ophunzira ace anadza, nampempha, nati, Mumuuze amuke; pakuti apfuula pambuyo pathu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 15
Onani Mateyu 15:23 nkhani