28 Pomwepo Yesu anayankha, nati kwa iye, Mkaziwe, cikhulupiriro cako ndi cacikuru; cikhale kwa iwe monga momwe wafunira. Ndipo mwana wace anacira nthawi yomweyo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 15
Onani Mateyu 15:28 nkhani