22 Ndipo Petro anamtenga Iye, nayamba kumdzudzula, kuti, Dzicitireni cifundo, Ambuye; sicidzatero kwa Inu ai.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:22 nkhani