23 Koma Iye anapotoloka, nati kwa Petro, Pita kumbuyo kwanga, Satana iwe; ndiwe condikhumudwitsa Ine; cifukwa sumasamalira za Mulungu, koma za anthu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:23 nkhani