24 Pomwepo Yesu anati kwa ophunzira ace, Ngati munthu afuna kudza pambuyo panga, adzikane yekha, natenge mtanda wace, nanditsate Ine.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:24 nkhani