4 Obadwa oipa ndi acigololo afunafuna cizindikiro; ndipo sadzalandira cizindikiro cina, koma cizindikiro ca Yona. Ndipo Iye anawasiya, nacokapo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 16
Onani Mateyu 16:4 nkhani