Mateyu 17:23 BL92

23 ndipo adzamupha Iye, ndipo Iye adzauka tsiku lacitatu. Ndipo iwo anali ndi cisoni cacikuru.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 17

Onani Mateyu 17:23 nkhani