Mateyu 17:24 BL92

24 Ndipo pofika ku Kapernao arnene aja akulandira ndalama za kukacisi anadza kwa Petro nati, Kodi Mphunzitsi wanu sapereka rupiyalo?

Werengani mutu wathunthu Mateyu 17

Onani Mateyu 17:24 nkhani