31 Cifukwa cace m'mene akapolo anzace anaona zocitidwazo, anagwidwa cisoni cacikuru, nadza, nalongosolera mbuye wao zonse zimene zinacitidwa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:31 nkhani