30 Ndipo iye sanafuna; koma anamuka, namponya iye m'nyumba yandende, kufikira abwezere ngongole.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 18
Onani Mateyu 18:30 nkhani