8 Iye ananena kwa iwo, Cifukwa ca kuuma mtima kwanu, Mose anakulolezani kucotsa akazi anu; koma paciyambi sikunakhala comweco.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 19
Onani Mateyu 19:8 nkhani