30 Ndipo onani, anthu akhungu awiri anakhala m'rnphepete mwa njira; m'mene iwo anamva kuti Yesu analikupitirirapo, anapfuula nati, Muticitire ife cifundo, Inu Mwana wa Davide.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 20
Onani Mateyu 20:30 nkhani